Levitiko 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake. Deuteronomo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+ Yesaya 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+
4 ndidzakugwetserani mvula pa nthawi yake.+ Nthaka idzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda idzakupatsani zipatso zake.
4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+
23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munadzala munthaka,+ ndipo chakudya chochokera munthakayo chidzakhala chochuluka komanso chopatsa thanzi.*+ Pa tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+