Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+ Yesaya 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+
10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+