Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+ Ezekieli 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine Yehova ndanena ndipo zidzachitikadi. Ndidzachitapo kanthu mosazengereza, popanda kumva chisoni kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako komanso zochita zako,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+
14 Ine Yehova ndanena ndipo zidzachitikadi. Ndidzachitapo kanthu mosazengereza, popanda kumva chisoni kapena kusintha maganizo.+ Iwo adzakuweruza mogwirizana ndi njira zako komanso zochita zako,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”