Yesaya 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano izi ndi zimene Yehova wanena,Mlengi wako iwe Yakobo, amene anakupanga iwe Isiraeli.+ Iye wanena kuti: “Usachite mantha, chifukwa ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina lako. Iwe ndiwe wanga. Zefaniya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsiku limenelo Yerusalemu adzauzidwa kuti: “Usaope iwe Ziyoni,+ Ndipo manja ako asafooke.
43 Tsopano izi ndi zimene Yehova wanena,Mlengi wako iwe Yakobo, amene anakupanga iwe Isiraeli.+ Iye wanena kuti: “Usachite mantha, chifukwa ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina lako. Iwe ndiwe wanga.