Levitiko 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musamabe,+ musamapusitse anzanu+ ndiponso musamachitirane chinyengo. Miyambo 12:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Choncho, popeza tsopano mwataya chinyengo, aliyense wa inu azilankhula zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo zolumikizana.+
19 Milomo imene imalankhula zoona idzakhalapo mpaka kalekale,+Koma lilime labodza lidzangokhalapo kwa kanthawi kochepa.+
25 Choncho, popeza tsopano mwataya chinyengo, aliyense wa inu azilankhula zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo zolumikizana.+