Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye, mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosauka.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+