-
Zekariya 5:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndatumiza mpukutuwo kuti ukalowe mʼnyumba ya munthu wakuba ndi mʼnyumba ya munthu wolumbira mwachinyengo mʼdzina langa. Mpukutuwo udzakhalabe mʼnyumba mwake nʼkuwonongeratu nyumbayo, matabwa ake ndi miyala yake.’”
-