Yesaya 35:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+ Yeremiya 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+
10 Anthu amene Yehova anawawombola adzabwerera+ ndipo adzafika ku Ziyoni akufuula mosangalala.+ Chisangalalo chosatha chidzakhala ngati chisoti chachifumu kumutu kwawo.+ Adzakhala okondwa ndi osangalalaNdipo chisoni ndi kubuula zidzachoka.+
12 Iwo adzabwera nʼkufuula mosangalala pamwamba pa phiri la Ziyoni.+Nkhope zawo zidzawala chifukwa cha ubwino wa* Yehova.Chifukwa cha mbewu, vinyo watsopano+ ndi mafuta,Ndiponso chifukwa cha ana a nkhosa ndi ana a ngʼombe.+ Iwo adzakhala ngati dimba lothiriridwa bwino+Ndipo sadzakhalanso ofooka.”+