Hagai 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzagonjetsa maufumu ndi kuchotsa mphamvu za maufumu a anthu a mitundu ina.+ Ndidzawononga magaleta* ndi okwera pamagaletawo. Mahatchi* ndi okwera pamahatchiwo adzaphedwa ndipo aliyense adzaphedwa ndi mʼbale wake ndi lupanga.’”+
22 Ndidzagonjetsa maufumu ndi kuchotsa mphamvu za maufumu a anthu a mitundu ina.+ Ndidzawononga magaleta* ndi okwera pamagaletawo. Mahatchi* ndi okwera pamahatchiwo adzaphedwa ndipo aliyense adzaphedwa ndi mʼbale wake ndi lupanga.’”+