Yesaya 44:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+ Yesaya 51:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+
22 Ndidzafafaniza zolakwa zako ndipo zidzakhala ngati ndaziphimba ndi mtambo+Ndipo machimo ako adzakhala ngati ndawaphimba ndi mtambo waukulu. Bwerera kwa ine, ndipo ine ndidzakuwombola.+
11 Anthu owomboledwa a Yehova adzabwerera.+ Adzabwera ku Ziyoni akufuula mosangalala,+Ndipo pamutu pawo padzakhala chisangalalo mpaka kalekale.+ Iwo adzapeza chisangalalo ndi chimwemwe,Ndipo chisoni komanso kulira zidzachoka.+