Yesaya 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova adzagawa pakati* chigawo cha* nyanja ya Iguputo,+Ndipo adzayendetsa dzanja lake moopseza Mtsinje.*+ Pogwiritsa ntchito mpweya* wake wotentha, adzamenya timitsinje 7 tamtsinjewo,*Ndipo adzachititsa anthu kuwoloka atavala nsapato zawo.
15 Yehova adzagawa pakati* chigawo cha* nyanja ya Iguputo,+Ndipo adzayendetsa dzanja lake moopseza Mtsinje.*+ Pogwiritsa ntchito mpweya* wake wotentha, adzamenya timitsinje 7 tamtsinjewo,*Ndipo adzachititsa anthu kuwoloka atavala nsapato zawo.