Mika 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu a mtundu uliwonse adzayenda mʼdzina la mulungu wawo.Koma ife tidzayenda mʼdzina la Yehova Mulungu+ wathu mpaka kalekale.
5 Anthu a mtundu uliwonse adzayenda mʼdzina la mulungu wawo.Koma ife tidzayenda mʼdzina la Yehova Mulungu+ wathu mpaka kalekale.