Ekisodo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina Lake molakwika osamulanga.+ Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza mʼdzina langa+ nʼkuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova.
7 Musagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wanu molakwika,+ chifukwa Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina Lake molakwika osamulanga.+