Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kusi anabereka Nimurodi, amene anali woyamba kukhala wamphamvu padziko lapansi.

  • Genesis 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ufumu wake unayambira ku* Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline mʼdziko la Sinara.+

  • Genesis 11:1, 2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tsopano dziko lonse lapansi linali ndi chilankhulo chimodzi ndipo anthu ankagwiritsa ntchito mawu ofanana. 2 Pamene anthuwo ankalowera chakumʼmawa, anapeza chigwa mʼdera la Sinara+ ndipo anayamba kukhala kumeneko.

  • Danieli 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Yehova anapereka Mfumu Yehoyakimu ya Yuda mʼmanja mwake,+ limodzi ndi zina mwa ziwiya za mʼnyumba ya* Mulungu woona. Nebukadinezara anatenga ziwiyazo nʼkupita nazo kudziko la Sinara,*+ kunyumba* ya mulungu wake ndipo anakaziika mʼnyumba yosungiramo chuma ya mulungu wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena