2 Mbiri 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Manase ndiponso anthu ake, koma iwo sanamvere.+ Yeremiya 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi ndilankhule ndi ndani nʼkumuchenjeza? Ndi ndani adzamvetsere? Taonani! Makutu awo ndi otseka,* choncho sangathe kumva.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala chinthu chimene akunyansidwa nacho+Ndipo sakusangalala nawo.
10 “Kodi ndilankhule ndi ndani nʼkumuchenjeza? Ndi ndani adzamvetsere? Taonani! Makutu awo ndi otseka,* choncho sangathe kumva.+ Taonani! Mawu a Yehova akhala chinthu chimene akunyansidwa nacho+Ndipo sakusangalala nawo.