Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Yehova ankachenjeza Aisiraeli ndi Ayuda kudzera mwa aneneri ake onse ndiponso amasomphenya onse+ kuti: “Siyani njira zanu zoipa+ ndipo muzisunga malamulo anga, mogwirizana ndi malamulo onse amene ndinalamula makolo anu ndiponso amene ndinakutumizirani kudzera mwa atumiki anga, aneneri.” 14 Koma iwo sanamvere ndipo anali ankhutukumve* ngati makolo awo amene sanasonyeze chikhulupiriro mwa Yehova Mulungu wawo.+

  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Uchititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+

      Uchititse makutu awo kuti asamamve,+

      Ndipo umate maso awo,

      Kuti asamaone ndi maso awowo,

      Ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo,

      Nʼcholinga choti mtima wawo usamvetse zinthu

      Komanso kuti asabwerere nʼkuchiritsidwa.”

  • Yeremiya 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 ‘Koma simunandimvere,’ akutero Yehova, ‘Mʼmalomwake munandikhumudwitsa ndi ntchito ya manja anu, zimene zinachititsa kuti tsoka likugwereni.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena