2 Mbiri 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo atangomaliza kupemphera,+ moto unatsika kuchokera kumwamba+ nʼkutentha nsembe yopsereza ndiponso nsembe zina ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza nyumbayo.+
7 Solomo atangomaliza kupemphera,+ moto unatsika kuchokera kumwamba+ nʼkutentha nsembe yopsereza ndiponso nsembe zina ndipo ulemerero wa Yehova unadzaza nyumbayo.+