Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ Machitidwe 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu okanika inu ndiponso osachita mdulidwe wamumtima ndi mʼmakutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mukuchita zinthu ngati mmene ankachitira makolo anu.+
7 Kumbukirani ndipo musamaiwale mmene munakwiyitsira Yehova Mulungu wanu mʼchipululu.+ Anthu inu mwakhala mukupandukira Yehova kuyambira tsiku limene munachoka mʼdziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
51 Anthu okanika inu ndiponso osachita mdulidwe wamumtima ndi mʼmakutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mukuchita zinthu ngati mmene ankachitira makolo anu.+