Yohane 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Muzikumbukira mawu amene ndinakuuzani aja: Kapolo sangakhale wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso mawu anu.
20 Muzikumbukira mawu amene ndinakuuzani aja: Kapolo sangakhale wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso mawu anu.