Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndi ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Komanso akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?” Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapereka chakudya kwa zinyama,+Amapatsa ana a makwangwala chakudya chimene akulirira.+ Mateyu 10:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+
41 Ndi ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Komanso akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?”
29 Mpheta ziwiri amazigulitsa kakhobidi kamodzi kochepa mphamvu,* si choncho? Koma palibe ngakhale imodzi imene idzagwa pansi Atate wanu osadziwa.+