Ekisodo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Ndikugwetserani chakudya kuchokera kumwamba ngati mvula,+ ndipo aliyense azitola muyezo womukwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese kuti ndione ngati angatsatire chilamulo changa kapena ayi.+ Ekisodo 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Mose anawauza kuti: “Aliyense asasiye chakudyachi mpaka mʼmawa.”+
4 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Ndikugwetserani chakudya kuchokera kumwamba ngati mvula,+ ndipo aliyense azitola muyezo womukwanira pa tsikulo.+ Ndikuchita izi kuti ndiwayese kuti ndione ngati angatsatire chilamulo changa kapena ayi.+