Luka 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Chifukwa mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa pachitsamba chaminga.
44 Chifukwa mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa pachitsamba chaminga.