Maliko 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anaitana ophunzira ake 12 aja nʼkuyamba kuwatumiza awiriawiri+ ndipo anawapatsa mphamvu kuti azitha kutulutsa mizimu yonyansa.+ Luka 9:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja nʼkuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse+ komanso kuti azitha kuchiritsa matenda.+ 2 Ndiyeno anawatumiza kuti azikalalikira za Ufumu wa Mulungu ndiponso kuchiritsa anthu.
7 Kenako anaitana ophunzira ake 12 aja nʼkuyamba kuwatumiza awiriawiri+ ndipo anawapatsa mphamvu kuti azitha kutulutsa mizimu yonyansa.+
9 Kenako Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja nʼkuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse+ komanso kuti azitha kuchiritsa matenda.+ 2 Ndiyeno anawatumiza kuti azikalalikira za Ufumu wa Mulungu ndiponso kuchiritsa anthu.