Mateyu 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma sanagone naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamupatsa dzina lakuti Yesu.+ Luka 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano mvetsera! Udzakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna+ ndipo udzamupatse dzina lakuti Yesu.+
31 Tsopano mvetsera! Udzakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna+ ndipo udzamupatse dzina lakuti Yesu.+