Luka 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Aliyense wofunitsitsa kuteteza moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake adzausunga.+ Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+
25 Aliyense amene amakonda moyo wake akuuwononga, koma aliyense amene amadana ndi moyo wake+ mʼdziko lino akuuteteza kuti adzapeze moyo wosatha.+