Mateyu 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma poyankha Mfumuyo idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, nthawi iliyonse imene munachitira zimenezo mmodzi wa abale anga aangʼono awa, munachitiranso ine.’+ Maliko 9:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+ Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
40 Koma poyankha Mfumuyo idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, nthawi iliyonse imene munachitira zimenezo mmodzi wa abale anga aangʼono awa, munachitiranso ine.’+
41 Komanso aliyense amene wakupatsani kapu ya madzi akumwa chifukwa chakuti ndinu ophunzira a Khristu,+ ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika.+
10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.