Mateyu 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kuuza ophunzira ake kuti iyeyo akuyenera kupita ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi ndipo akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+ Mateyu 17:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri. Mateyu 27:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 nʼkunena kuti: “Bwana, ife takumbukira kuti munthu wachinyengo uja adakali moyo ananena kuti, ‘Pakadzadutsa masiku atatu ndidzaukitsidwa.’+ Luka 24:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+
21 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kuuza ophunzira ake kuti iyeyo akuyenera kupita ku Yerusalemu. Kumeneko akazunzidwa kwambiri ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi ndipo akaphedwa, koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.+
23 ndipo adzamupha. Koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Atamva zimenezi iwo anamva chisoni kwambiri.
63 nʼkunena kuti: “Bwana, ife takumbukira kuti munthu wachinyengo uja adakali moyo ananena kuti, ‘Pakadzadutsa masiku atatu ndidzaukitsidwa.’+
46 ndipo anawauza kuti, “Malemba amanena kuti: Khristu adzazunzika ndipo tsiku lachitatu adzauka kwa akufa,+