Mateyu 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+ Maliko 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+ Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+
29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
25 Chifukwa amene ali nazo adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.”+
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Chifukwa amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+