Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 12:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo, kuti asamaone ndi maso awowo, kuti mitima yawo isamvetse zinthu nʼkutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+

  • Aroma 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+

  • 2 Akorinto 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba pangano lakale likamawerengedwa,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena