Luka 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, siyani kudera nkhawa za moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa za matupi anu kuti mudzavala chiyani.+
22 Kenako anauza ophunzira ake kuti: “Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, siyani kudera nkhawa za moyo wanu kuti mudzadya chiyani kapena kudera nkhawa za matupi anu kuti mudzavala chiyani.+