Mateyu 24:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika. Aroma 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma ndifunse kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “mawu awo anamveka padziko lonse lapansi, ndipo uthenga wawo unamveka mpaka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+ Akolose 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 umene unafika kwa inu. Uthenga wabwino ukubala zipatso ndiponso kufalikira padziko lonse.+ Zimenezi ndi zimenenso zakhala zikuchitika kwa inu kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu komwe ndi kwenikweni.
14 Ndipo uthenga wabwino uwu wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi kumene kuli anthu, kuti ukhale umboni kwa anthu amitundu yonse,+ kenako mapeto adzafika.
18 Koma ndifunse kuti, Kodi kumva sanamve? Pajatu “mawu awo anamveka padziko lonse lapansi, ndipo uthenga wawo unamveka mpaka kumalekezero a dziko lapansi kumene kuli anthu.”+
6 umene unafika kwa inu. Uthenga wabwino ukubala zipatso ndiponso kufalikira padziko lonse.+ Zimenezi ndi zimenenso zakhala zikuchitika kwa inu kuyambira tsiku limene munamva ndi kudziwa molondola za kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu komwe ndi kwenikweni.