-
Afilipi 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Zoonadi, ndimaona kuti zinthu zonse nʼzosapindulitsa chifukwa chakuti ndinadziwa Khristu Yesu Ambuye wanga, chimene ndi chinthu chamtengo wapatali kwambiri. Chifukwa cha iye, ndinataya zinthu zonse ndipo ndimaziona ngati mulu wa zinyalala, kuti ndikhale pa ubwenzi weniweni ndi Khristu,
-