Maliko 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho chimene Mulungu wachimanga pamodzi,* munthu asachilekanitse.”+ 1 Akorinto 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma ngati angamusiye, akhale choncho wosakwatiwa. Apo ayi, abwererane ndi mwamuna wakeyo. Mwamunanso asasiye mkazi wake.+
11 Koma ngati angamusiye, akhale choncho wosakwatiwa. Apo ayi, abwererane ndi mwamuna wakeyo. Mwamunanso asasiye mkazi wake.+