1 Akorinto 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo. Komabe aliyense ali ndi mphatso+ imene Mulungu anamupatsa ndipo timamutumikira mʼnjira zosiyanasiyana.
7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo. Komabe aliyense ali ndi mphatso+ imene Mulungu anamupatsa ndipo timamutumikira mʼnjira zosiyanasiyana.