-
Maliko 10:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Tsopano anapitiriza ulendo wawo wopita ku Yerusalemu ndipo Yesu anali patsogolo pawo. Ophunzirawo anadabwa kwambiri ndipo anthu amene ankamutsatirawo anayamba kuchita mantha. Kachiwirinso anatengera pambali ophunzira 12 aja nʼkuyamba kuwauza zinthu izi zimene zinali zitatsala pangʼono kuti zimuchitikire:+
-