-
Maliko 10:39, 40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Iwo anayankha kuti: “Inde tingatero.” Atatero Yesu anawauza kuti: “Zimene ine ndikumwa mudzamwadi ndipo mudzabatizidwadi ubatizo umene ine ndikubatizidwa.+ 40 Koma si ine woyenera kusankha amene adzakhale kudzanja langa lamanja kapena lamanzere. Atate wanga adzapereka mwayi umenewo kwa anthu amene anawakonzera.”
-