Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Choncho aliyense amene adzadzichepetse ngati mwana wamngʼonoyu ndi amene adzakhale wamkulu kwambiri mu Ufumu wakumwamba.+

  • Mateyu 23:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma wamkulu kwambiri pakati panu akhale mtumiki wanu.+

  • Maliko 10:43, 44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Sizikuyenera kukhala choncho pakati panu. Koma aliyense amene akufuna kuti akhale wamkulu pakati panu akuyenera kukhala mtumiki wanu+ 44 ndipo amene akufuna kuti akhale woyamba pakati panu akuyenera kukhala kapolo wa onse.

  • Luka 22:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Inu musakhale otero.+ Koma amene ali wamkulu kwambiri pa nonsenu akhale ngati wamngʼono+ kwambiri pa nonsenu, ndipo amene ali mtsogoleri akhale ngati wotumikira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena