-
Malaki 2:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Wansembe ayenera kuphunzitsa anthu za Mulungu. Anthu ayenera kupita kwa iye kuti akamve Chilamulo*+ chifukwa iye ndi mthenga wa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
8 Koma inu mwasiya kuyenda panjira yoyenera. Mwachititsa kuti anthu ambiri asiye kutsatira Chilamulo.*+ Ndipo mwaphwanya pangano limene ndinachita ndi Levi,”+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-