Luka 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho iye anawauza kuti: “Inu ndi amene mumanena pamaso pa anthu kuti ndinu olungama,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene anthu amachiona kuti ndi chapamwamba ndi chonyansa pamaso pa Mulungu.+
15 Choncho iye anawauza kuti: “Inu ndi amene mumanena pamaso pa anthu kuti ndinu olungama,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene anthu amachiona kuti ndi chapamwamba ndi chonyansa pamaso pa Mulungu.+