Mateyu 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho mukamapereka mphatso zachifundo,* musamalize lipenga ngati mmene amachitira anthu achinyengo mʼmasunagoge ndi mʼmisewu nʼcholinga choti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.
2 Choncho mukamapereka mphatso zachifundo,* musamalize lipenga ngati mmene amachitira anthu achinyengo mʼmasunagoge ndi mʼmisewu nʼcholinga choti anthu awatamande. Ndithu ndikukuuzani, anthu amenewo akulandiriratu mphoto yawo yonse.