Luka 11:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Tsoka kwa inu, chifukwa mumamanga manda* a aneneri, komatu makolo anu ndi amene anawapha!+