Luka 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma zinthu zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani nʼkukuzunzani+ ndipo adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakupititsani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+
12 Koma zinthu zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani nʼkukuzunzani+ ndipo adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakupititsani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+