-
1 Mafumu 9:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba imene ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga.+ Aisiraeli adzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ 8 Nyumbayi idzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi adzayangʼana modabwa ndipo adzaimba mluzu nʼkunena kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani Yehova anachitira zimenezi dzikoli komanso nyumbayi?’+
-
-
Mateyu 21:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Nʼchifukwa chake ndikukuuzani kuti, Ufumu wa Mulungu udzachotsedwa kwa inu nʼkuperekedwa ku mtundu wobereka zipatso zake.
-