1 Atesalonika 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho tisapitirize kugona ngati mmene ena onse akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+ 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani tcheru+ chifukwa mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda ngati mkango wobangula, kuti ameze winawake.*+
6 Choncho tisapitirize kugona ngati mmene ena onse akuchitira,+ koma tikhalebe maso+ ndipo tikhalebe oganiza bwino.+
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani tcheru+ chifukwa mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda ngati mkango wobangula, kuti ameze winawake.*+