-
Luka 16:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Munthu amene ndi wokhulupirika pa chinthu chachingʼono amakhalanso wokhulupirika pa chinthu chachikulu, ndipo munthu amene ndi wosakhulupirika pa chinthu chachingʼono amakhalanso wosakhulupirika pa chinthu chachikulu.
-