Luka 19:18, 19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako kunabwera wachiwiri ndipo anati, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija yapindula ndalama zina zokwana ma mina 5.’+ 19 Iye anauzanso ameneyu kuti, ‘Nawenso ukhala woyangʼanira mizinda 5.’
18 Kenako kunabwera wachiwiri ndipo anati, ‘Mbuyanga, ndalama yanu ya mina ija yapindula ndalama zina zokwana ma mina 5.’+ 19 Iye anauzanso ameneyu kuti, ‘Nawenso ukhala woyangʼanira mizinda 5.’