Aroma 2:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ 7 Adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene akupitirizabe kuchita zabwino.+ Anthu amenewa akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosawonongeka.
6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ 7 Adzapereka moyo wosatha kwa anthu amene akupitirizabe kuchita zabwino.+ Anthu amenewa akuyesetsa kupeza ulemerero, ulemu ndi moyo wosawonongeka.