Ekisodo 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30 kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ngʼombeyo iziphedwa mwa kuiponya miyala. Zekariya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti nʼzoyenera, ndipatseni malipiro anga. Koma ngati mukuona kuti nʼzosayenera musandipatse.” Iwo anandilipira* ndalama 30 zasiliva.+ Mateyu 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yudasi amene anamupereka uja, ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima moti anapita kukabweza ndalama 30 zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.+
32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30 kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ngʼombeyo iziphedwa mwa kuiponya miyala.
12 Kenako ndinawauza kuti: “Ngati mukuona kuti nʼzoyenera, ndipatseni malipiro anga. Koma ngati mukuona kuti nʼzosayenera musandipatse.” Iwo anandilipira* ndalama 30 zasiliva.+
3 Kenako Yudasi amene anamupereka uja, ataona kuti Yesu waweruzidwa kuti aphedwe, anavutika koopsa mumtima moti anapita kukabweza ndalama 30 zasiliva zija kwa ansembe aakulu ndiponso akulu.+