Maliko 14:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma mmodzi mwa anthu amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+ Luka 22:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Mmodzi wa iwo anatemadi kapolo wa mkulu wa ansembe nʼkuduliratu khutu lake lakumanja.+ Yohane 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Simoni Petulo, amene anali ndi lupanga, analisolola nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Kapoloyo dzina lake anali Makasi.
47 Koma mmodzi mwa anthu amene anaimirira chapafupi anasolola lupanga lake nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake.+
10 Kenako Simoni Petulo, amene anali ndi lupanga, analisolola nʼkutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe mpaka kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Kapoloyo dzina lake anali Makasi.