Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliko 16:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Tsiku la Sabata+ litatha, Mariya wa ku Magadala, Mariya+ mayi wa Yakobo ndi Salome anagula zonunkhiritsa kuti akapake thupi la Yesu.+

  • Luka 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Koma pa tsiku loyamba la mlungu, azimayi aja analawirira mʼmawa kwambiri kupita kumandako,* atatenga zonunkhira zimene anakonza zija.+

  • Luka 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Azimayiwa anali Mariya wa ku Magadala, Jowana ndi Mariya amayi ake a Yakobo. Komanso azimayi ena onse amene anali nawo limodzi ankauza atumwi zinthu zimenezi.

  • Yohane 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsiku loyamba la mlunguwo, Mariya wa ku Magadala anapita kumandako* mʼmawa kwambiri,+ kudakali mdima, ndipo anaona kuti mwala wachotsedwa kale pamandawo.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena